Machitidwe 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 nʼkunena kuti: “Iwe munthu wodzaza ndi chinyengo chamtundu uliwonse ndiponso zoipa, mwana wa Mdyerekezi+ komanso mdani wa chinthu chilichonse cholungama, kodi udzasiya liti kupotoza njira zowongoka za Yehova?*
10 nʼkunena kuti: “Iwe munthu wodzaza ndi chinyengo chamtundu uliwonse ndiponso zoipa, mwana wa Mdyerekezi+ komanso mdani wa chinthu chilichonse cholungama, kodi udzasiya liti kupotoza njira zowongoka za Yehova?*