Machitidwe 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Bwanamkubwa uja ataona zimenezi, anakhala wokhulupirira, chifukwa anadabwa kwambiri ndi zimene anaphunzira zokhudza Yehova.* Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:12 Nsanja ya Olonda,9/1/1986, tsa. 24
12 Bwanamkubwa uja ataona zimenezi, anakhala wokhulupirira, chifukwa anadabwa kwambiri ndi zimene anaphunzira zokhudza Yehova.*