Machitidwe 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Paulo ndi anzakewo, anayamba ulendo wa panyanja kuchoka ku Pafo, ndipo anakafika ku Pega, ku Pamfuliya. Koma Yohane+ anawasiya nʼkubwerera ku Yerusalemu.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:13 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 88-89 Nsanja ya Olonda,3/15/2010, tsa. 7
13 Kenako Paulo ndi anzakewo, anayamba ulendo wa panyanja kuchoka ku Pafo, ndipo anakafika ku Pega, ku Pamfuliya. Koma Yohane+ anawasiya nʼkubwerera ku Yerusalemu.+