Machitidwe 13:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chilamulo ndi zimene aneneri analemba zitawerengedwa pamaso pa anthu,+ atsogoleri a sunagoge anatuma munthu kukawauza kuti: “Abale inu, ngati muli ndi mawu alionse amene angalimbikitse anthuwa, lankhulani.”
15 Chilamulo ndi zimene aneneri analemba zitawerengedwa pamaso pa anthu,+ atsogoleri a sunagoge anatuma munthu kukawauza kuti: “Abale inu, ngati muli ndi mawu alionse amene angalimbikitse anthuwa, lankhulani.”