Machitidwe 13:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mulungu wa anthu awa Aisiraeli, anasankha makolo athu akale. Pamene iwo ankakhala mʼdziko lachilendo la Iguputo, iye anawasandutsa mtundu wamphamvu, ndipo anawatulutsa mʼdzikomo ndi dzanja lake lamphamvu.+
17 Mulungu wa anthu awa Aisiraeli, anasankha makolo athu akale. Pamene iwo ankakhala mʼdziko lachilendo la Iguputo, iye anawasandutsa mtundu wamphamvu, ndipo anawatulutsa mʼdzikomo ndi dzanja lake lamphamvu.+