Machitidwe 13:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo atawononga mitundu 7 ya anthu mʼdziko la Kanani, anapereka dzikolo kwa Aisiraeli kuti likhale cholowa chawo.+
19 Ndipo atawononga mitundu 7 ya anthu mʼdziko la Kanani, anapereka dzikolo kwa Aisiraeli kuti likhale cholowa chawo.+