Machitidwe 13:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma pamene Yohane ankamaliza utumiki wake, ankanena kuti, ‘Kodi mukuganiza kuti ndine ndani? Amene mukumuganizirayo si ine ayi. Koma wina akubwera pambuyo panga, amene ine si woyenera kumasula nsapato zake.’+
25 Koma pamene Yohane ankamaliza utumiki wake, ankanena kuti, ‘Kodi mukuganiza kuti ndine ndani? Amene mukumuganizirayo si ine ayi. Koma wina akubwera pambuyo panga, amene ine si woyenera kumasula nsapato zake.’+