Machitidwe 13:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Anthu inu, abale anga, inu mbadwa za Abulahamu, ndi anthu onse oopa Mulungu amene muli nawo pamodziwa, mawu a chipulumutso chimenechi atumizidwa kwa ife.+
26 Anthu inu, abale anga, inu mbadwa za Abulahamu, ndi anthu onse oopa Mulungu amene muli nawo pamodziwa, mawu a chipulumutso chimenechi atumizidwa kwa ife.+