Machitidwe 13:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Chifukwa anthu a ku Yerusalemu ndi olamulira awo sanamuzindikire. Koma pamene ankamuweruza, anakwaniritsa zimene aneneri ananena,+ zomwe zimawerengedwa mokweza sabata lililonse. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:27 Nsanja ya Olonda,3/1/1986, ptsa. 29-30
27 Chifukwa anthu a ku Yerusalemu ndi olamulira awo sanamuzindikire. Koma pamene ankamuweruza, anakwaniritsa zimene aneneri ananena,+ zomwe zimawerengedwa mokweza sabata lililonse.