Machitidwe 13:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndipo kwa masiku ambiri anaonekera kwa anthu amene anayenda naye kuchokera ku Galileya kupita ku Yerusalemu. Panopa amenewa ndi mboni zake kwa anthu.+
31 Ndipo kwa masiku ambiri anaonekera kwa anthu amene anayenda naye kuchokera ku Galileya kupita ku Yerusalemu. Panopa amenewa ndi mboni zake kwa anthu.+