Machitidwe 13:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Dziwaninso kuti pa zinthu zonse zimene kunali kosatheka kuti muonedwe opanda mlandu kudzera mʼChilamulo cha Mose,+ aliyense wokhulupirira akuonedwa wopanda mlandu kudzera mwa iyeyu.+
39 Dziwaninso kuti pa zinthu zonse zimene kunali kosatheka kuti muonedwe opanda mlandu kudzera mʼChilamulo cha Mose,+ aliyense wokhulupirira akuonedwa wopanda mlandu kudzera mwa iyeyu.+