Machitidwe 13:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 ‘Inu onyoza onani zimene ine ndikuchita nʼkudabwa nazo. Kenako mudzatha, chifukwa simudzakhulupirira ngakhale pangʼono zimene ndidzachite mʼmasiku anu, ngakhale wina atakufotokozerani mwatsatanetsatane.’”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:41 Nsanja ya Olonda,2/1/2000, tsa. 136/1/1991, tsa. 22
41 ‘Inu onyoza onani zimene ine ndikuchita nʼkudabwa nazo. Kenako mudzatha, chifukwa simudzakhulupirira ngakhale pangʼono zimene ndidzachite mʼmasiku anu, ngakhale wina atakufotokozerani mwatsatanetsatane.’”+