Machitidwe 13:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Choncho msonkhano wamʼsunagoge utatha, Ayuda ndi anthu ambiri omwe analowa Chiyuda amene ankalambira Mulungu anatsatira Paulo ndi Baranaba. Ndipo iwo anauza anthuwo kuti apitirize kukhala oyenera kulandira kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu.+
43 Choncho msonkhano wamʼsunagoge utatha, Ayuda ndi anthu ambiri omwe analowa Chiyuda amene ankalambira Mulungu anatsatira Paulo ndi Baranaba. Ndipo iwo anauza anthuwo kuti apitirize kukhala oyenera kulandira kukoma mtima kwakukulu kwa Mulungu.+