Machitidwe 13:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ayuda ataona gulu la anthulo, anachita nsanje ndipo anayamba kutsutsa mwamwano zimene Paulo ankalankhula.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:45 Nsanja ya Olonda,6/15/1990, tsa. 11
45 Ayuda ataona gulu la anthulo, anachita nsanje ndipo anayamba kutsutsa mwamwano zimene Paulo ankalankhula.+