Machitidwe 13:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Choncho Paulo ndi Baranaba analankhula molimba mtima kuti: “Inu munali oyenera kuti muyambe kuuzidwa mawu a Mulungu.+ Koma popeza mukuwakana ndipo mukudziweruza nokha kuti ndinu osayenera moyo wosatha, ife tikupita kwa anthu a mitundu ina.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:46 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 90-92
46 Choncho Paulo ndi Baranaba analankhula molimba mtima kuti: “Inu munali oyenera kuti muyambe kuuzidwa mawu a Mulungu.+ Koma popeza mukuwakana ndipo mukudziweruza nokha kuti ndinu osayenera moyo wosatha, ife tikupita kwa anthu a mitundu ina.+