Machitidwe 13:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Koma Ayuda anauza zoipa amayi otchuka oopa Mulungu komanso amuna olemekezeka amumzindawo. Choncho iwo anachititsa kuti Paulo ndi Baranaba ayambe kuzunzidwa+ ndipo anawaponya kunja kwa mzinda wawo. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:50 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 91 Nsanja ya Olonda,6/15/1990, tsa. 11
50 Koma Ayuda anauza zoipa amayi otchuka oopa Mulungu komanso amuna olemekezeka amumzindawo. Choncho iwo anachititsa kuti Paulo ndi Baranaba ayambe kuzunzidwa+ ndipo anawaponya kunja kwa mzinda wawo.