Machitidwe 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho kwa nthawi yaitali, ankalankhula molimba mtima chifukwa cha mphamvu ya Yehova.* Iye anatsimikizira mawu a kukoma mtima kwake kwakukulu, polola kuti ophunzirawo azichita zizindikiro ndi zodabwitsa.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:3 Nsanja ya Olonda,12/1/1998, tsa. 16
3 Choncho kwa nthawi yaitali, ankalankhula molimba mtima chifukwa cha mphamvu ya Yehova.* Iye anatsimikizira mawu a kukoma mtima kwake kwakukulu, polola kuti ophunzirawo azichita zizindikiro ndi zodabwitsa.+