-
Machitidwe 14:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Koma gulu la anthu mumzindawo linagawanika. Ena anali kumbali ya Ayuda, ena kumbali ya atumwi.