Machitidwe 14:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno anthu a mitundu ina komanso Ayuda pamodzi ndi olamulira awo, anakonza chiwembu kuti achitire chipongwe atumwiwo nʼkuwaponya miyala.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:5 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 95-96
5 Ndiyeno anthu a mitundu ina komanso Ayuda pamodzi ndi olamulira awo, anakonza chiwembu kuti achitire chipongwe atumwiwo nʼkuwaponya miyala.+