Machitidwe 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma iwo atadziwitsidwa zimenezi, anathawira mʼmizinda ya Lukaoniya, Lusitara, Debe, ndi mʼmadera ozungulira.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:6 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 95-96 Nsanja ya Olonda,6/1/1993, tsa. 36/15/1990, tsa. 11
6 Koma iwo atadziwitsidwa zimenezi, anathawira mʼmizinda ya Lukaoniya, Lusitara, Debe, ndi mʼmadera ozungulira.+