Machitidwe 14:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Gulu la anthu litaona zimene Paulo anachitazo, linafuula mʼchilankhulo cha Chilukaoniya kuti: “Milungu yakhala ngati anthu ndipo yatsikira kwa ife!”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:11 Nsanja ya Olonda,6/15/1990, ptsa. 11-12
11 Gulu la anthu litaona zimene Paulo anachitazo, linafuula mʼchilankhulo cha Chilukaoniya kuti: “Milungu yakhala ngati anthu ndipo yatsikira kwa ife!”+