Machitidwe 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Komabe iye sanangokhala wopanda umboni+ wakuti anachita zabwino. Anakupatsani mvula kuchokera kumwamba ndi nyengo zimene zokolola zanu zimakhala zambiri.+ Anadzaza mitima yanu ndi chakudya komanso chisangalalo.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:17 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 97-98 Yandikirani, ptsa. 272-273 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 7 Galamukani!,No. 3 2021 tsa. 14 Nsanja ya Olonda,7/1/2013, tsa. 116/15/1990, ptsa. 11-12
17 Komabe iye sanangokhala wopanda umboni+ wakuti anachita zabwino. Anakupatsani mvula kuchokera kumwamba ndi nyengo zimene zokolola zanu zimakhala zambiri.+ Anadzaza mitima yanu ndi chakudya komanso chisangalalo.”+
14:17 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 97-98 Yandikirani, ptsa. 272-273 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 7 Galamukani!,No. 3 2021 tsa. 14 Nsanja ya Olonda,7/1/2013, tsa. 116/15/1990, ptsa. 11-12