Machitidwe 14:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Mʼmalo onsewa ankalimbitsa ophunzira+ komanso kuwathandiza kuti apitirize kukhala ndi chikhulupiriro. Ankawauza kuti: “Tiyenera kukumana ndi mavuto ambiri kuti tikalowe mu Ufumu wa Mulungu.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:22 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo, Nsanja ya Olonda,11/1/2015, ptsa. 13-149/15/2014, tsa. 13
22 Mʼmalo onsewa ankalimbitsa ophunzira+ komanso kuwathandiza kuti apitirize kukhala ndi chikhulupiriro. Ankawauza kuti: “Tiyenera kukumana ndi mavuto ambiri kuti tikalowe mu Ufumu wa Mulungu.”+