Machitidwe 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Anasankhanso akulu mumpingo uliwonse,+ ndipo atapemphera komanso kusala kudya,+ anawapereka kwa Yehova* yemwe anamukhulupirira. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:23 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 99
23 Anasankhanso akulu mumpingo uliwonse,+ ndipo atapemphera komanso kusala kudya,+ anawapereka kwa Yehova* yemwe anamukhulupirira.