Machitidwe 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Atafika kumeneko anasonkhanitsa anthu amumpingo ndipo anawafotokozera zinthu zambiri zimene Mulungu anachita kudzera mwa iwo. Anawafotokozeranso kuti Mulungu anatsegulanso khomo kuti anthu a mitundu ina akhale okhulupirira.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 14:27 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 101
27 Atafika kumeneko anasonkhanitsa anthu amumpingo ndipo anawafotokozera zinthu zambiri zimene Mulungu anachita kudzera mwa iwo. Anawafotokozeranso kuti Mulungu anatsegulanso khomo kuti anthu a mitundu ina akhale okhulupirira.+