-
Machitidwe 15:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Atafika ku Yerusalemu analandiridwa ndi manja awiri ndi mpingo, atumwi komanso akulu. Ndipo anafotokoza zinthu zambiri zimene Mulungu anachita kudzera mwa iwowo.
-