Machitidwe 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma okhulupirira ena, amene kale anali mʼgulu lampatuko la Afarisi, anaimirira mʼmipando yawo nʼkunena kuti: “Mʼpofunika kuwadula komanso kuwalamula kuti azisunga Chilamulo cha Mose.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:5 Kuchitira Umboni Mokwanira, ptsa. 105, 107
5 Koma okhulupirira ena, amene kale anali mʼgulu lampatuko la Afarisi, anaimirira mʼmipando yawo nʼkunena kuti: “Mʼpofunika kuwadula komanso kuwalamula kuti azisunga Chilamulo cha Mose.”+