Machitidwe 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 ‘Zimenezi zikadzatha ndidzabwerera nʼkumanganso tenti* ya Davide imene inagwa. Ndidzamanganso malo ogumuka a nyumbayo nʼkuikonzanso. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:16 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 109 Nsanja ya Olonda,2/15/2013, ptsa. 8-96/15/1990, tsa. 13
16 ‘Zimenezi zikadzatha ndidzabwerera nʼkumanganso tenti* ya Davide imene inagwa. Ndidzamanganso malo ogumuka a nyumbayo nʼkuikonzanso.