Machitidwe 15:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzachita zimenezi kuti anthu otsalawo afunefune Yehova* ndi mtima wonse. Amufunefune pamodzi ndi mitundu yonse ya anthu, anthu otchedwa ndi dzina langa, watero Yehova* amene akuchita zinthu zimenezi,+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:17 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 109 Nsanja ya Olonda,1/15/2012, tsa. 5
17 Ndidzachita zimenezi kuti anthu otsalawo afunefune Yehova* ndi mtima wonse. Amufunefune pamodzi ndi mitundu yonse ya anthu, anthu otchedwa ndi dzina langa, watero Yehova* amene akuchita zinthu zimenezi,+