Machitidwe 15:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako atumwi ndi akulu pamodzi ndi mpingo wonse, anagwirizana zosankha amuna pakati pawo, kuti awatumize ku Antiokeya limodzi ndi Paulo ndi Baranaba. Choncho anasankha Yudasi wotchedwa Barasaba ndi Sila,+ omwe ankatsogolera abale. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:22 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 113 Nsanja ya Olonda,2/15/1999, ptsa. 26-27
22 Kenako atumwi ndi akulu pamodzi ndi mpingo wonse, anagwirizana zosankha amuna pakati pawo, kuti awatumize ku Antiokeya limodzi ndi Paulo ndi Baranaba. Choncho anasankha Yudasi wotchedwa Barasaba ndi Sila,+ omwe ankatsogolera abale.