-
Machitidwe 15:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Amuna amenewa atanyamuka, anapita ku Antiokeya. Kumeneko anasonkhanitsa gulu lonse la anthu nʼkuwapatsa kalatayo.
-