Machitidwe 15:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Koma Paulo ndi Baranaba anatsala ku Antiokeya. Iwo pamodzi ndi anthu enanso ambiri ankaphunzitsa komanso kulengeza uthenga wabwino wa mawu a Yehova.*
35 Koma Paulo ndi Baranaba anatsala ku Antiokeya. Iwo pamodzi ndi anthu enanso ambiri ankaphunzitsa komanso kulengeza uthenga wabwino wa mawu a Yehova.*