Machitidwe 15:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Patapita masiku, Paulo anauza Baranaba kuti: “Tiyeni tibwerere kumizinda yonse kumene tinalalikira mawu a Yehova* kuti tikachezere abale ndiponso tikawaone kuti ali bwanji.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:36 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 119
36 Patapita masiku, Paulo anauza Baranaba kuti: “Tiyeni tibwerere kumizinda yonse kumene tinalalikira mawu a Yehova* kuti tikachezere abale ndiponso tikawaone kuti ali bwanji.”+