Machitidwe 15:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Koma Paulo anasankha Sila, ndipo abale atamupempherera Pauloyo kuti Yehova* amusonyeze kukoma mtima kwakukulu, ananyamuka.+
40 Koma Paulo anasankha Sila, ndipo abale atamupempherera Pauloyo kuti Yehova* amusonyeze kukoma mtima kwakukulu, ananyamuka.+