Machitidwe 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mtsikana ameneyu ankangotsatira Paulo ndi ifeyo nʼkumafuula kuti: “Anthu awa ndi akapolo a Mulungu Wamʼmwambamwamba+ ndipo akulengeza njira ya chipulumutso kwa inu.” Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:17 Nsanja ya Olonda,4/1/1994, tsa. 316/15/1990, tsa. 16
17 Mtsikana ameneyu ankangotsatira Paulo ndi ifeyo nʼkumafuula kuti: “Anthu awa ndi akapolo a Mulungu Wamʼmwambamwamba+ ndipo akulengeza njira ya chipulumutso kwa inu.”