-
Machitidwe 16:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Popeza kuti anamulamula zimenezi, iye anakawaika mʼchipinda chamkati cha ndendeyo nʼkumanga mapazi awo mʼmatangadza.
-