Machitidwe 16:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mwadzidzidzi panachitika chivomerezi champhamvu, mpaka maziko a ndendeyo anagwedezeka. Nthawi yomweyo zitseko zonse zinatseguka, ndipo aliyense unyolo wake unamasuka.+
26 Mwadzidzidzi panachitika chivomerezi champhamvu, mpaka maziko a ndendeyo anagwedezeka. Nthawi yomweyo zitseko zonse zinatseguka, ndipo aliyense unyolo wake unamasuka.+