-
Machitidwe 16:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Iye anapempha kuti amupatse nyale ndipo mwamsanga analowa mkatimo. Akunjenjemera ndi mantha, anagwada patsogolo pa Paulo ndi Sila.
-