-
Machitidwe 16:34Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
34 Kenako anapita nawo kunyumba kwake nʼkuwaikira chakudya patebulo. Ndipo iye limodzi ndi onse a mʼbanja lake, anasangalala kwambiri chifukwa anakhulupirira Mulungu.
-