Machitidwe 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo anthu amene anaperekeza Paulo anakamufikitsa ku Atene. Koma anabwerera atatumidwa kuti akauze Sila ndi Timoteyo+ kuti atsatire Pauloyo mwamsanga. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 17:15 Nsanja ya Olonda,10/15/2004, tsa. 196/15/1990, tsa. 18
15 Ndipo anthu amene anaperekeza Paulo anakamufikitsa ku Atene. Koma anabwerera atatumidwa kuti akauze Sila ndi Timoteyo+ kuti atsatire Pauloyo mwamsanga.