-
Machitidwe 17:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Atalowa mʼsunagoge anayamba kukambirana ndi Ayuda ndi anthu ena opembedza Mulungu. Ndipo tsiku ndi tsiku ankakambirananso ndi anthu amene ankawapeza pamsika.
-