-
Machitidwe 17:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Choncho anamugwira nʼkupita naye kubwalo la Areopagi nʼkumuuza kuti: “Kodi tingadziweko za chiphunzitso chatsopano chimene ukuphunzitsachi?
-