Machitidwe 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kumeneko anapeza Myuda wina dzina lake Akula,+ wa ku Ponto. Iyeyu pamodzi ndi mkazi wake Purisila, anali atangofika kumene kuchokera ku Italy, chifukwa Kalaudiyo anali atalamula Ayuda onse kuti achoke ku Roma. Choncho Paulo anapita kunyumba kwawo. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:2 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 137 Galamukani!,4/2011, tsa. 12 Nsanja ya Olonda,11/15/2003, ptsa. 19-2012/15/1996, tsa. 226/15/1990, ptsa. 18-19 Mawu a Mulungu, tsa. 62
2 Kumeneko anapeza Myuda wina dzina lake Akula,+ wa ku Ponto. Iyeyu pamodzi ndi mkazi wake Purisila, anali atangofika kumene kuchokera ku Italy, chifukwa Kalaudiyo anali atalamula Ayuda onse kuti achoke ku Roma. Choncho Paulo anapita kunyumba kwawo.
18:2 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 137 Galamukani!,4/2011, tsa. 12 Nsanja ya Olonda,11/15/2003, ptsa. 19-2012/15/1996, tsa. 226/15/1990, ptsa. 18-19 Mawu a Mulungu, tsa. 62