Machitidwe 18:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma iwo atapitiriza kumutsutsa ndiponso kumunyoza, iye anakutumula zovala zake+ nʼkuwauza kuti: “Magazi anu akhale pamutu panu.+ Ine ndilibe mlandu.+ Kuyambira panopa ndizipita kwa anthu a mitundu ina.”+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:6 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 151 Nsanja ya Olonda,10/1/1996, ptsa. 21-22
6 Koma iwo atapitiriza kumutsutsa ndiponso kumunyoza, iye anakutumula zovala zake+ nʼkuwauza kuti: “Magazi anu akhale pamutu panu.+ Ine ndilibe mlandu.+ Kuyambira panopa ndizipita kwa anthu a mitundu ina.”+