-
Machitidwe 18:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Koma pamene Paulo ankati azitsegula pakamwa, Galiyo anauza Ayudawo kuti: “Ayuda inu, chikanakhala cholakwa china kapena mlandu waukulu, ndithu ndikanaleza mtima nʼkukumvetserani.
-