Machitidwe 18:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Atakhala kumeneko kwa kanthawi, ananyamuka nʼkuyamba kuyenda malo osiyanasiyana mʼchigawo cha Galatiya ndi Fulugiya+ ndipo ankalimbikitsa ophunzira onse.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:23 Kuchitira Umboni Mokwanira, tsa. 160
23 Atakhala kumeneko kwa kanthawi, ananyamuka nʼkuyamba kuyenda malo osiyanasiyana mʼchigawo cha Galatiya ndi Fulugiya+ ndipo ankalimbikitsa ophunzira onse.+