Machitidwe 18:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Tsopano Myuda wina dzina lake Apolo,+ wa ku Alekizandiriya, amene ankalankhula mwaluso, anafika ku Efeso. Iyeyu ankadziwanso bwino Malemba. Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:24 Nsanja ya Olonda,10/1/1996, ptsa. 20-21
24 Tsopano Myuda wina dzina lake Apolo,+ wa ku Alekizandiriya, amene ankalankhula mwaluso, anafika ku Efeso. Iyeyu ankadziwanso bwino Malemba.