Machitidwe 18:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chifukwa iye anawatsimikizira Ayuda poyera komanso mwamphamvu kuti anali olakwa, ndipo anagwiritsa ntchito Malemba posonyeza kuti Yesu ndiyedi Khristu.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:28 Nsanja ya Olonda,10/1/1996, ptsa. 21-22
28 Chifukwa iye anawatsimikizira Ayuda poyera komanso mwamphamvu kuti anali olakwa, ndipo anagwiritsa ntchito Malemba posonyeza kuti Yesu ndiyedi Khristu.+