Machitidwe 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndipo anawafunsa kuti: “Kodi munalandira mzimu woyera mutakhala okhulupirira?”+ Iwo anamuyankha kuti: “Ifetu sitinamvepo kuti kuli mzimu woyera.”
2 ndipo anawafunsa kuti: “Kodi munalandira mzimu woyera mutakhala okhulupirira?”+ Iwo anamuyankha kuti: “Ifetu sitinamvepo kuti kuli mzimu woyera.”