Machitidwe 19:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kwa miyezi itatu, Paulo ankapita kusunagoge+ kumene ankalankhula molimba mtima. Kumeneko ankakamba nkhani ndiponso kuwafotokozera mfundo zogwira mtima zokhudza Ufumu wa Mulungu.+ Machitidwe Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:8 Muzikonda Anthu, lesson 7
8 Kwa miyezi itatu, Paulo ankapita kusunagoge+ kumene ankalankhula molimba mtima. Kumeneko ankakamba nkhani ndiponso kuwafotokozera mfundo zogwira mtima zokhudza Ufumu wa Mulungu.+